2 Mafumu 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumuyo inalamula anthu onse kuti: “Chitirani Pasika+ Yehova Mulungu wanu, mogwirizana ndi zimene zalembedwa mʼbuku la panganoli.”+
21 Mfumuyo inalamula anthu onse kuti: “Chitirani Pasika+ Yehova Mulungu wanu, mogwirizana ndi zimene zalembedwa mʼbuku la panganoli.”+