2 Mafumu 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho atumiki ake ananyamula mtembo wake pagaleta kuchokera ku Megido nʼkupita nawo ku Yerusalemu ndipo anakamuika mʼmanda ake. Kenako anthu amʼdzikolo anatenga Yehoahazi mwana wa Yosiya nʼkumudzoza ndiponso kumuveka ufumu mʼmalo mwa bambo ake.+ 2 Mbiri 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nʼchifukwa chake ndidzakuika mʼmanda a makolo ako ndipo udzaikidwa mʼmanda ako mwamtendere. Maso ako sadzaona tsoka lonse lomwe ndidzabweretse pamalo ano ndi anthu ake.’”’”+ Kenako iwo anakauza mfumuyo zimenezi.
30 Choncho atumiki ake ananyamula mtembo wake pagaleta kuchokera ku Megido nʼkupita nawo ku Yerusalemu ndipo anakamuika mʼmanda ake. Kenako anthu amʼdzikolo anatenga Yehoahazi mwana wa Yosiya nʼkumudzoza ndiponso kumuveka ufumu mʼmalo mwa bambo ake.+
28 Nʼchifukwa chake ndidzakuika mʼmanda a makolo ako ndipo udzaikidwa mʼmanda ako mwamtendere. Maso ako sadzaona tsoka lonse lomwe ndidzabweretse pamalo ano ndi anthu ake.’”’”+ Kenako iwo anakauza mfumuyo zimenezi.