-
Yeremiya 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti,
‘Chitani zinthu mozindikira.
Itanani akazi oimba nyimbo zoimba polira kuti abwere.+
Ndipo tumizani anthu kuti akaitane akazi odziwa kulira maliro,
-