2 Samueli 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Gadi anapita kwa Davide tsiku lomwelo nʼkukamuuza kuti: “Pitani mukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna wa Chiyebusi.”+ 1 Mbiri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Undigulitse* malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe kuti mliriwu uthe pakati pa anthuwa.+ Undiuze ndalama zake zonse.”
18 Kenako Gadi anapita kwa Davide tsiku lomwelo nʼkukamuuza kuti: “Pitani mukamangire Yehova guwa lansembe pamalo opunthira mbewu a Arauna wa Chiyebusi.”+
22 Kenako Davide anauza Orinani kuti: “Undigulitse* malo ako opunthira mbewuwa kuti ndimangirepo Yehova guwa lansembe kuti mliriwu uthe pakati pa anthuwa.+ Undiuze ndalama zake zonse.”