2 Mafumu 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mʼchaka cha 5 cha Yehoramu+ mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, pamene Yehosafati anali mfumu ya Yuda, Yehoramu+ mwana wa Yehosafati mfumu ya Yuda, anakhala mfumu.
16 Mʼchaka cha 5 cha Yehoramu+ mwana wa Ahabu mfumu ya Isiraeli, pamene Yehosafati anali mfumu ya Yuda, Yehoramu+ mwana wa Yehosafati mfumu ya Yuda, anakhala mfumu.