-
2 Mafumu 9:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Kenako Yehu anakwera galeta lake nʼkunyamuka ulendo wa ku Yezereeli popeza Yehoramu anali chigonere kumeneko chifukwa chovulala. Ahaziya mfumu ya Yuda anali atapita ku Yezereeli komweko kukaona Yehoramu.
-