Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ukadzamwalira+ nʼkugona mʼmanda ndi makolo ako, ndidzachititsa kuti mbadwa* yako, mwana wako weniweni, akhale mfumu ndipo ndidzachititsa kuti ufumu wake ukhazikike.+ 13 Iye ndi amene adzamangire dzina langa nyumba,+ ndipo ndidzakhazikitsa mpando wake wachifumu mpaka kalekale.+

  • 1 Mafumu 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komabe, chifukwa cha kukhulupirika kwa Davide,+ Yehova Mulungu wake anamʼpatsa nyale mu Yerusalemu+ pokweza mwana wake pambuyo pake ndiponso pochititsa kuti Yerusalemu akhalepobe.

  • 2 Mbiri 21:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Yehova sanafune kuwononga nyumba ya Davide chifukwa cha pangano limene anachita ndi Davide,+ poti anamulonjeza kuti adzamʼpatsa nyale nthawi zonse, iyeyo ndi ana ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena