Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako Yehova anachititsa+ kuti Afilisiti+ ndi Aluya,+ amene anali pafupi ndi Aitiyopiya, aukire Yehoramu.

  • 2 Mbiri 21:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yehoramu anakhala mfumu ali ndi zaka 32 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8. Iye atafa, palibe amene anadandaula. Choncho anamuika mu Mzinda wa Davide,+ koma osati mʼmanda a mafumu.+

  • 2 Mbiri 28:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako Ahazi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mumzinda wa Yerusalemu. Iye sanaikidwe mʼmanda a mafumu a Isiraeli.+ Ndiyeno Hezekiya mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena