2 Mafumu 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atumiki ake amene anamupha anali Yozakara mwana wa Simeyati ndi Yehozabadi mwana wa Someri.+ Zitatero anamuika mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide ndipo Amaziya mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.+
21 Atumiki ake amene anamupha anali Yozakara mwana wa Simeyati ndi Yehozabadi mwana wa Someri.+ Zitatero anamuika mʼmanda a makolo ake mu Mzinda wa Davide ndipo Amaziya mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.+