2 Mafumu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mʼchaka chachiwiri cha Yehoasi+ mwana wa Yehoahazi mfumu ya Isiraeli, Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, anakhala mfumu. 2 Mafumu 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova, koma osati ngati Davide+ kholo lake. Anachita zonse ngati mmene Yehoasi bambo ake anachitira.+
14 Mʼchaka chachiwiri cha Yehoasi+ mwana wa Yehoahazi mfumu ya Isiraeli, Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, anakhala mfumu.
3 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova, koma osati ngati Davide+ kholo lake. Anachita zonse ngati mmene Yehoasi bambo ake anachitira.+