-
2 Mbiri 11:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Rehobowamu ankakhala ku Yerusalemu, ndipo anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri mʼdziko la Yuda.
-
-
2 Mbiri 11:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Mʼmizinda yonse anaikamo zishango zazikulu ndi mikondo ingʼonoingʼono. Mizindayo anailimbitsa kwambiri ndipo iye anapitiriza kulamulira Yuda ndi Benjamini.
-