Numeri 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Nthawi zonse mukamasamutsa chihema, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, Alevi ndi amene azimanga chihemacho. Munthu aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+
51 Nthawi zonse mukamasamutsa chihema, Aleviwo azichipasula,+ ndipo mukafika pomanga msasa, Alevi ndi amene azimanga chihemacho. Munthu aliyense amene si Mlevi akayandikira chihemacho aziphedwa.+