Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 11:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Aleviwo anasiya malo awo odyetserako ziweto ndi madera awo+ nʼkupita ku Yuda ndi ku Yerusalemu, chifukwa Yerobowamu ndi ana ake anachotsa Aleviwo pa udindo wokhala ansembe a Yehova.+

  • 2 Mbiri 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma anthu a mʼmafuko onse a Isiraeli amene anali ndi mtima wofunafuna Yehova Mulungu wa Isiraeli, anatsatira ansembe ku Yerusalemu kukapereka nsembe kwa Yehova Mulungu wa makolo awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena