Zekariya 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukatenge siliva ndi golide nʼkupangira chisoti chachifumu.* Chisoticho udzaveke Yoswa+ mkulu wa ansembe, mwana wa Yehozadaki.
11 Ukatenge siliva ndi golide nʼkupangira chisoti chachifumu.* Chisoticho udzaveke Yoswa+ mkulu wa ansembe, mwana wa Yehozadaki.