Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano akuluakulu a Ayuda anapitiriza kumanga ndipo ntchitoyo inkayenda bwino+ chifukwa cholimbikitsidwa ndi ulosi wa mneneri Hagai+ ndi Zekariya+ mdzukulu wa Ido. Iwo anamanga nyumbayo nʼkuimaliza potsatira lamulo la Mulungu wa Isiraeli+ ndi lamulo la Koresi,+ Dariyo+ komanso Aritasasita mfumu ya Perisiya.+

  • Hagai 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 ‘Koma tsopano limba mtima iwe Zerubabele. Limba mtima iwe Yoswa mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe,’ watero Yehova.

      ‘Limbani mtima anthu nonse amʼdzikoli+ ndipo gwirani ntchito,’ watero Yehova.

      ‘Pakuti ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.

  • Hagai 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Uza Zerubabele bwanamkubwa wa Yuda kuti, ‘Ine ndigwedeza kumwamba ndi dziko lapansi.+

  • Zekariya 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ngakhale Zerubabele+ atakumana ndi chopinga chachikulu ngati phiri, chidzasalazidwa nʼkukhala malo afulati.+ Iye adzabweretsa mwala wotsiriza ndipo anthu adzafuula kuti: “Koma mwalawu ndiye ndi wokongola bwanji! Koma ndiye ndi wokongola!”’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena