Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ezara anabwera kuchokera ku Babulo. Iye anali wokopera* Malemba ndipo ankadziwa bwino* Chilamulo cha Mose+ chimene Yehova Mulungu wa Isiraeli anapereka. Mfumu inamupatsa zonse zimene anapempha chifukwa dzanja la Yehova Mulungu wake linkamuthandiza.

  • Ezara 7:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Iye wandisonyeza chikondi chokhulupirika pamaso pa mfumu,+ pamaso pa alangizi ake+ ndiponso pamaso pa akalonga onse amphamvu a mfumu. Ineyo ndinalimba mtima* chifukwa dzanja la Yehova Mulungu wanga linkandithandiza, ndipo ndinasonkhanitsa atsogoleri a Aisiraeli kuti tipitire limodzi.

  • Ezara 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndinachita manyazi kupempha asilikali kwa mfumu ndi okwera pamahatchi kuti atiteteze kwa adani mʼnjira, chifukwa tinali titauza mfumuyo kuti: “Dzanja labwino la Mulungu wathu limathandiza anthu onse omufunafuna,+ koma amasonyeza mkwiyo ndi mphamvu zake kwa onse omusiya.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena