Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hagai 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Mʼchaka chachiwiri cha ulamuliro wa Mfumu Dariyo, mʼmwezi wa 6, pa tsiku loyamba la mweziwo, mawu a Yehova anafika kwa Zerubabele+ yemwe anali bwanamkubwa wa Yuda mwana wa Salatiyeli, ndiponso kwa Yoswa yemwe anali mkulu wa ansembe mwana wa Yehozadaki. Mawuwa anafika kwa anthu amenewa kudzera mwa mneneri Hagai*+ kuti:

  • Hagai 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Choncho Yehova analimbikitsa+ Zerubabele mwana wa Salatiyeli bwanamkubwa wa Yuda,+ Yoswa+ mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe ndiponso anthu ena onse. Ndipo iwo anabwera nʼkuyamba kugwira ntchito panyumba ya Mulungu wawo, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena