Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Anthu amene ankamanga nyumbayo anamaliza kumanga maziko a kachisi wa Yehova.+ Atatero, ansembe ovala zovala zaunsembe omwe ananyamula malipenga+ ndiponso Alevi, ana a Asafu omwe ananyamula zinganga, anaimirira kuti atamande Yehova motsatira dongosolo limene Davide mfumu ya Isiraeli anakhazikitsa.+

  • Hagai 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ‘Lero, pa tsiku la 24 la mwezi wa 9, pamene maziko a kachisi wa Yehova ayalidwa,+ kuyambira lero kupita mʼtsogolo, chonde ganizirani izi mofatsa:

  • Zekariya 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Manja a Zerubabele anayala maziko a nyumbayi+ ndipo manja ake omwewo adzaimalizitsa.+ Ndipo mudzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa inu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena