-
Nehemiya 9:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Tsopano inu Mulungu wathu, Mulungu wamkulu, wamphamvu, wochititsa mantha, wosunga pangano komanso wachikondi chokhulupirika,+ musachepetse mavuto amene tikukumana nawo ifeyo, mafumu athu, akalonga athu,+ ansembe athu,+ aneneri athu,+ makolo athu ndi anthu anu onse kuyambira mu nthawi ya mafumu a Asuri+ mpaka pano.
-