Nehemiya 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo chifukwa cha chifundo chanu chachikulu simunawafafanize+ kapena kuwasiya, popeza ndinu Mulungu wachisomo ndi wachifundo.+ Salimo 138:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale nditakumana ndi mavuto, inu mudzandithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.+ Mumagwiritsa ntchito mphamvu zanu polimbana ndi adani anga omwe ndi okwiya.Dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.
31 Ndipo chifukwa cha chifundo chanu chachikulu simunawafafanize+ kapena kuwasiya, popeza ndinu Mulungu wachisomo ndi wachifundo.+
7 Ngakhale nditakumana ndi mavuto, inu mudzandithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.+ Mumagwiritsa ntchito mphamvu zanu polimbana ndi adani anga omwe ndi okwiya.Dzanja lanu lamanja lidzandipulumutsa.