1 Mbiri 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Magulu a alonda apageti+ anali awa: Pa mbadwa za Kora panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu. Ezara 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+ Ezara 2:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana a alonda apageti:+ ana a Salumu, ana a Ateri, ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita ndi ana a Sobai, onse analipo 139.
26 Magulu a alonda apageti+ anali awa: Pa mbadwa za Kora panali Meselemiya,+ mwana wa Kore wochokera mwa ana a Asafu.
2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+
42 Ana a alonda apageti:+ ana a Salumu, ana a Ateri, ana a Talimoni,+ ana a Akubu,+ ana a Hatita ndi ana a Sobai, onse analipo 139.