Ezara 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa ana a Elamu+ panali Mataniya, Zekariya, Yehiela,+ Abidi, Yeremoti ndi Eliya. Ezara 10:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Onsewa anatenga akazi achilendo+ ndipo akaziwo ndi ana awo anawatumiza kwawo.+