1 Mbiri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+ 1 Mbiri 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Alonda apageti+ anali Salumu, Akubu, Talimoni ndi Ahimani ndipo mʼbale wawo Salumu ndi amene anali mtsogoleri. Nehemiya 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alonda apageti anali Akubu, Talimoni+ ndi abale awo amene ankalondera mʼmageti. Onse pamodzi analipo 172. Nehemiya 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ ankalondera mageti.+ Iwo ankalondera zipinda zosungira zinthu zomwe zinali pafupi ndi mageti.
2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+
17 Alonda apageti+ anali Salumu, Akubu, Talimoni ndi Ahimani ndipo mʼbale wawo Salumu ndi amene anali mtsogoleri.
19 Alonda apageti anali Akubu, Talimoni+ ndi abale awo amene ankalondera mʼmageti. Onse pamodzi analipo 172.
25 Mataniya,+ Bakibukiya, Obadiya, Mesulamu, Talimoni ndi Akubu+ ankalondera mageti.+ Iwo ankalondera zipinda zosungira zinthu zomwe zinali pafupi ndi mageti.