Yoswa 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nawonso anthu a ku Gibiyoni+ anamva zimene Yoswa anachita ku Yeriko+ ndi ku Ai.+ Yoswa 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma pa tsikuli, Yoswa anawalamula kuti azitunga madzi ndi kutola nkhuni za Aisiraeli onse+ ndiponso zapaguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.+ Nehemiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atumiki apakachisi*+ omwe ankakhala ku Ofeli+ anakonza mpandawo mpaka patsogolo pa Geti la Kumadzi,+ kumʼmawa. Iwo anakonzanso nsanja yomwe inatulukira kunja kwa mpanda.
27 Koma pa tsikuli, Yoswa anawalamula kuti azitunga madzi ndi kutola nkhuni za Aisiraeli onse+ ndiponso zapaguwa lansembe la Yehova, pamalo alionse amene Mulungu wasankha.+ Iwo akhala akuchita zimenezi mpaka lero.+
26 Atumiki apakachisi*+ omwe ankakhala ku Ofeli+ anakonza mpandawo mpaka patsogolo pa Geti la Kumadzi,+ kumʼmawa. Iwo anakonzanso nsanja yomwe inatulukira kunja kwa mpanda.