1 Mbiri 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide, komanso Zadoki+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo mʼmagulu mogwirizana ndi udindo wa utumiki wawo. 1 Mbiri 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 a 7 Hakozi, a 8 Abiya,+ Nehemiya 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Meremoti+ mwana wa Uliya, mwana wa Hakozi, anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera pageti la nyumba ya Eliyasibu mpaka pamene nyumbayo inathera.
3 Davide, komanso Zadoki+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo mʼmagulu mogwirizana ndi udindo wa utumiki wawo.
21 Meremoti+ mwana wa Uliya, mwana wa Hakozi, anakonza gawo lina la mpandawo kuchokera pageti la nyumba ya Eliyasibu mpaka pamene nyumbayo inathera.