Levitiko 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wansembe azivala zovala zake zogwirira ntchito+ komanso azivala kabudula wansalu+ wobisa* thupi lake. Kenako azichotsa phulusa*+ la nsembe yopsereza imene yawotchedwa pamoto wapaguwalo ndipo aziika phulusalo pambali pa guwa lansembe.
10 Wansembe azivala zovala zake zogwirira ntchito+ komanso azivala kabudula wansalu+ wobisa* thupi lake. Kenako azichotsa phulusa*+ la nsembe yopsereza imene yawotchedwa pamoto wapaguwalo ndipo aziika phulusalo pambali pa guwa lansembe.