Nehemiya 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho chifukwa cha zimenezi, tikuchita pangano lodalirika+ lochita kulemba ndipo akalonga athu, Alevi athu ndi ansembe athu atsimikizira panganoli ndi chidindo chawo.”+
38 Choncho chifukwa cha zimenezi, tikuchita pangano lodalirika+ lochita kulemba ndipo akalonga athu, Alevi athu ndi ansembe athu atsimikizira panganoli ndi chidindo chawo.”+