-
1 Mbiri 9:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Pa mbadwa za Benjamini panali Salelu mwana wa Mesulamu. Mesulamu anali mwana wa Hodaviya ndipo Hodaviya anali mwana wa Hasenuwa.
-