1 Samueli 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anamufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani uli wekhawekha?”+
21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anamufunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani uli wekhawekha?”+