1 Mbiri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Elipaala anali Ebere, Misamu, Semedi (amene anamanga mzinda wa Ono+ ndi wa Lodi+ ndiponso midzi yake yozungulira), Ezara 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+ Ezara 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ana a Lodi, Hadidi ndi Ono, 725.
12 Ana a Elipaala anali Ebere, Misamu, Semedi (amene anamanga mzinda wa Ono+ ndi wa Lodi+ ndiponso midzi yake yozungulira),
2 Awa ndi anthu amʼchigawo* amene anatuluka mu ukapolo+ pa anthu omwe Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo anawatengera ku Babulo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense kumzinda wakwawo.+