Ezara 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati kuti abweretse ziwiyazo nʼkuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda. Ezara 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ziwiya zonse zagolide ndi zasiliva zinalipo 5,400. Sezibazara anatenga zinthu zonsezi pamene anthu amene anagwidwa ukapolo+ ankachoka ku Babulo kupita ku Yerusalemu.
8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati kuti abweretse ziwiyazo nʼkuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.
11 Ziwiya zonse zagolide ndi zasiliva zinalipo 5,400. Sezibazara anatenga zinthu zonsezi pamene anthu amene anagwidwa ukapolo+ ankachoka ku Babulo kupita ku Yerusalemu.