Nehemiya 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndinayendabe mpaka kukafika ku Geti la Kukasupe+ ndi ku Dziwe la Mfumu. Koma kunalibe njira yoti chiweto chimene ndinakwerapo chidutse.
14 Ndinayendabe mpaka kukafika ku Geti la Kukasupe+ ndi ku Dziwe la Mfumu. Koma kunalibe njira yoti chiweto chimene ndinakwerapo chidutse.