-
Ezara 6:16, 17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ndiyeno Aisiraeli, ansembe, Alevi+ ndi anthu ena onse amene anachokera ku ukapolo, anatsegulira nyumba ya Mulunguyo mosangalala. 17 Iwo anapereka nsembe ngʼombe zamphongo 100, nkhosa zamphongo 200 ndi ana a nkhosa amphongo 400. Anaperekanso mbuzi zamphongo 12 za nsembe yamachimo ya Aisiraeli onse, mogwirizana ndi chiwerengero cha mafuko a Isiraeli.+
-