Ekisodo 34:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zipatso zoyamba kucha zabwino kwambiri zamʼmunda mwanu muzibwera nazo kunyumba ya Yehova Mulungu wanu.+ Musamawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi ake.”+ Numeri 15:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukupititsani, 19 muzikapereka chopereka kwa Yehova pa chakudya chilichonse chamʼdzikolo,+ chimene muzikadya. Deuteronomo 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 mukatenge zina mwa zipatso zoyambirira pa zokolola* zonse zamʼmunda mwanu zimene mudzakolole mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani. Mukaziike mʼdengu nʼkupita nazo kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuika dzina lake.+
26 Zipatso zoyamba kucha zabwino kwambiri zamʼmunda mwanu muzibwera nazo kunyumba ya Yehova Mulungu wanu.+ Musamawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi ake.”+
18 “Lankhula ndi Aisiraeli ndipo uwauze kuti, ‘Mukakalowa mʼdziko limene ndikukupititsani, 19 muzikapereka chopereka kwa Yehova pa chakudya chilichonse chamʼdzikolo,+ chimene muzikadya.
2 mukatenge zina mwa zipatso zoyambirira pa zokolola* zonse zamʼmunda mwanu zimene mudzakolole mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani. Mukaziike mʼdengu nʼkupita nazo kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuika dzina lake.+