Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ndi ansembe anzake ndiponso Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi abale ake, anakamanga guwa lansembe la Mulungu wa Isiraeli. Anachita zimenezi kuti aziperekerapo nsembe zopsereza, mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼChilamulo cha Mose,+ munthu wa Mulungu woona.

  • Hagai 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli,+ Yoswa mwana wa Yehozadaki+ mkulu wa ansembe ndiponso anthu ena onse anamvera mawu a Yehova Mulungu wawo ndi a mneneri Hagai, chifukwa Yehova Mulungu wawo ndi amene anamutuma. Ndipo anthuwo anayamba kuchita mantha chifukwa cha Yehova.

  • Luka 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamene Yesu+ anayamba ntchito yake anali ndi zaka pafupifupi 30.+ Anthu ankadziwa kuti Yesu anali mwana

      wa Yosefe,+

      mwana wa Heli,

  • Luka 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 mwana wa Yoanani,

      mwana wa Resa,

      mwana wa Zerubabele,+

      mwana wa Salatiyeli,+

      mwana wa Neri,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena