Ezara 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zitachitika, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, Ezara*+ anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku Babulo. Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+ Nehemiya 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mʼmwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inkafuna vinyo choncho ndinatenga vinyoyo nʼkukapereka kwa mfumu ngati mmene ndinkachitira nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.
7 Zimenezi zitachitika, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, Ezara*+ anabwera ku Yerusalemu kuchokera ku Babulo. Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+
2 Mʼmwezi wa Nisani,* mʼchaka cha 20+ cha mfumu Aritasasita,+ mfumuyo inkafuna vinyo choncho ndinatenga vinyoyo nʼkukapereka kwa mfumu ngati mmene ndinkachitira nthawi zonse.+ Koma ndinali ndisanakhalepo wachisoni pamaso pake.