Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako ndinawauza kuti: “Inu mukuona vuto lalikulu limene tili nalo. Yerusalemu ndi bwinja ndipo mageti ake anatenthedwa ndi moto. Tiyeni timangenso mpanda wa Yerusalemu kuti anthu asiye kutinyoza.”

  • Maliro 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Misewu yopita ku Ziyoni ikulira chifukwa palibe amene akupita kuchikondwerero.+

      Mageti ake onse awonongedwa.+ Ansembe ake akuusa moyo.

      Anamwali* ake agwidwa ndi chisoni ndipo iyeyo akumva ululu mumtima.

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena