Esitere 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa tsikuli, Mfumu Ahasiwero anapereka kwa Mfumukazi Esitere nyumba ya Hamani,+ yemwe anali mdani wa Ayuda.+ Ndipo Moredikayi anapita kwa mfumu chifukwa Esitere anali atafotokozera mfumuyo chibale chomwe chinali pakati pawo.+
8 Pa tsikuli, Mfumu Ahasiwero anapereka kwa Mfumukazi Esitere nyumba ya Hamani,+ yemwe anali mdani wa Ayuda.+ Ndipo Moredikayi anapita kwa mfumu chifukwa Esitere anali atafotokozera mfumuyo chibale chomwe chinali pakati pawo.+