-
Esitere 8:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mʼmakalatawo mfumu inapereka chilolezo kwa Ayuda mʼmizinda yosiyanasiyana kuti asonkhane nʼcholinga choti adziteteze komanso aphe asilikali a gulu lililonse kapena chigawo chilichonse amene angawaukire, kuphatikizapo akazi ndi ana nʼkutenga zinthu zawo.+ 12 Zimenezi zinkayenera kuchitika mʼzigawo zonse za Mfumu Ahasiwero pa tsiku la 13 lomwelo la mwezi wa 12 umene ndi mwezi wa Adara.*+
-