15 Ndiyeno Moredikayi anachoka pamaso pa mfumu atavala chovala chachifumu chansalu yabuluu ndi yoyera. Analinso atavala chipewa chachikulu chachifumu chagolide ndiponso mkanjo wa nsalu yabwino kwambiri yaubweya wa nkhosa wapepo.+ Ndipo anthu amumzinda wa Susani anafuula chifukwa chosangalala.