Esitere 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimene analemba mʼmakalatawo anazipereka kuti zikhale lamulo mʼzigawo zonse. Analengeza kwa anthu a mitundu yonse nʼcholinga choti Ayuda akonzekere kudzabwezera adani awo pa tsiku limeneli.+ Salimo 149:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakamwa pawo patuluke nyimbo zotamanda Mulungu,Ndipo lupanga lakuthwa konsekonse likhale mʼmanja mwawo, 7 Kuti abwezere anthu a mitundu ina,Komanso kupereka chilango kwa mitundu ya anthu,
13 Zimene analemba mʼmakalatawo anazipereka kuti zikhale lamulo mʼzigawo zonse. Analengeza kwa anthu a mitundu yonse nʼcholinga choti Ayuda akonzekere kudzabwezera adani awo pa tsiku limeneli.+
6 Pakamwa pawo patuluke nyimbo zotamanda Mulungu,Ndipo lupanga lakuthwa konsekonse likhale mʼmanja mwawo, 7 Kuti abwezere anthu a mitundu ina,Komanso kupereka chilango kwa mitundu ya anthu,