Esitere 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Esitere anayankha kuti: “Ngati mungavomereze mfumu,+ bwanji mawa Ayuda amene ali ku Susani* achitenso zimene lamulo laleroli likunena?+ Ndikupemphanso kuti ana aamuna 10 a Hamani apachikidwe pamtengo.”+ Esitere 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Ayuda amene anali ku Susani* anasonkhananso pa tsiku la 14 la mwezi wa Adara,+ ndipo anapha amuna 300 ku Susani, koma sanatenge zinthu zawo.
13 Esitere anayankha kuti: “Ngati mungavomereze mfumu,+ bwanji mawa Ayuda amene ali ku Susani* achitenso zimene lamulo laleroli likunena?+ Ndikupemphanso kuti ana aamuna 10 a Hamani apachikidwe pamtengo.”+
15 Ndiyeno Ayuda amene anali ku Susani* anasonkhananso pa tsiku la 14 la mwezi wa Adara,+ ndipo anapha amuna 300 ku Susani, koma sanatenge zinthu zawo.