-
Esitere 5:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho mkazi wake Zeresi ndiponso anzake onsewo anamuuza kuti: “Mukonzetse mtengo wautali mikono 50.* Ndiyeno mawa mʼmawa mukauze mfumu kuti Moredikayi apachikidwe pamtengowo.+ Mukatero mukapite ndi mfumu kuphwandoko kukasangalala.” Hamani anaona kuti maganizo amenewa ndi abwino, choncho anakonzetsa mtengowo.
-
-
Esitere 7:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Choncho Hamani anamupachika pamtengo umene anakonzera Moredikayi, ndipo mkwiyo wa mfumu unatha.
-