2 Mbiri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.
3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.