-
Yobu 11:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ngati ukuchita chinachake cholakwika, usiyiretu kuchichita,
Ndipo usalole kuti mʼmatenti ako mukhale zinthu zopanda chilungamo.
-
-
Yobu 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Masiku a moyo wako adzakhala owala kuposa masana,
Ngakhale usiku udzakhala ngati mʼmawa.
-