Genesis 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pambuyo pake, Harana anamwalira mumzinda wa Uri+ womwe ndi wa Akasidi,+ kumene anabadwira. Anamwalira bambo ake Tera ali ndi moyo.
28 Pambuyo pake, Harana anamwalira mumzinda wa Uri+ womwe ndi wa Akasidi,+ kumene anabadwira. Anamwalira bambo ake Tera ali ndi moyo.