Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 13:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ndiyangʼaneni ndipo mundiyankhe, inu Yehova Mulungu wanga.

      Chititsani maso anga kuti aone kuwala, kuti ndisagone mu imfa.

  • Yohane 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atanena zimenezi, anauza ophunzira akewo kuti: “Mnzathu Lazaro ali mʼtulo,+ koma ndikupita kumeneko kukamudzutsa.”

  • Machitidwe 7:59, 60
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 59 Pamene ankamuponya miyala, Sitefano anapempha mochonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.” 60 Kenako anagwada nʼkufuula ndi mawu amphamvu kuti: “Yehova,* musawaimbe mlandu wa tchimo ili.”+ Atanena zimenezi anafa.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena