Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako Abisalomu ndi amuna onse a Isiraeli anati: “Malangizo a Husai mbadwa ya Areki ndi abwino+ kusiyana ndi a Ahitofeli.”+ Yehova anaonetsetsa kuti anthuwo asatsatire malangizo a Ahitofeli ngakhale kuti anali abwino. Yehova anachita zimenezi kuti abweretsere Abisalomu tsoka.+

  • Yesaya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Uchititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+

      Uchititse makutu awo kuti asamamve,+

      Ndipo umate maso awo,

      Kuti asamaone ndi maso awowo,

      Ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo,

      Nʼcholinga choti mtima wawo usamvetse zinthu

      Komanso kuti asabwerere nʼkuchiritsidwa.”

  • Mateyu 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pa nthawi imeneyo Yesu ananena kuti: “Ndikukutamandani inu Atate pamaso pa onse, Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa anthu anzeru ndi ozindikira mwawabisira zinthu zimenezi ndipo mwaziulula kwa ana aangʼono.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena