Yobu 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amamva phokoso lochititsa mantha mʼmakutu ake,+Pa nthawi yamtendere achifwamba amamuukira. Yobu 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Adzazula muvi kumsana kwake,Komanso chida chonyezimira pandulu yake,Ndipo mantha adzamugwira.+