Salimo 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Mulungu wanga, ine ndimakuitanani masana, koma simundiyankha.+Ndipo usiku sindikhala chete, ndimaitanabe. Habakuku 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Inu Yehova, kodi ndidzalirira thandizo koma inu osandimva mpaka liti?+ Kodi ndidzapempha thandizo kuti mundipulumutse ku chiwawa koma inu osachitapo kanthu mpaka liti?+
2 Inu Mulungu wanga, ine ndimakuitanani masana, koma simundiyankha.+Ndipo usiku sindikhala chete, ndimaitanabe.
2 “Inu Yehova, kodi ndidzalirira thandizo koma inu osandimva mpaka liti?+ Kodi ndidzapempha thandizo kuti mundipulumutse ku chiwawa koma inu osachitapo kanthu mpaka liti?+